MEC iyamba kukonzekera zisankho za 2025
….A Chilima akuzadziwa ngati akudzayima pa 18 Juni, 2025 …Nyumba ya Malamulo ikudzayimitsidwa pa 16 Juni, 2025 …Kalembera wapadera achitika mu Novembala Nthawi yokonzekera chisankho cha mu 2025 yayambika pamene…