NOCMA, MERA akolezera chipwirikiti cha mafuta: Kampani ya Addax itchulidwa
Zadziwika kuti kampani yoyenga mafuta ya Addax Petroleum ndiyo inatumiza mkulu wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) a Henry Kachaje kupita ku Dubai kuti akachite zokambirana ndi mtsogoleri…