Skip to content
July 14, 2025
  • Malawi 2025: Women Register to Vote, Men Register Excuses
  • International Conservetionists shocked with Chakweras pardon of criminil gangs
  • UK Sattar’s case set for  Sept 2027
  • Tungwa’s Talking Pen

Newsletter
Random News
  • About Us
  • Business
  • Arts & Entertainment
  • Politics
  • iElections
  • Languages
    • Yao
    • Chichewa
    • Tumbuka
  • Sports
Headlines
  • Malawi 2025: Women Register to Vote, Men Register Excuses

    2 days ago2 days ago
  • International Conservetionists shocked with Chakweras pardon of criminil gangs

    2 weeks ago2 weeks ago
  • UK Sattar’s case set for  Sept 2027

    2 weeks ago2 weeks ago
  • Tungwa’s Talking Pen

    2 weeks ago2 weeks ago
  • DPP convention: Ex-Ministers to battle for key positions

    12 months ago12 months ago
  • MCP out to destabilise UTM

    12 months ago12 months ago
  • Home
  • Languages

Languages

  • Chichewa
  • Languages
  • World

Boma likuganizila kuphazi-Alimi a fodya

admin3 weeks ago3 weeks ago08 mins

..fodya chaka chino wochepa kale ndi 60 million kgs …25% yotenga boma idzutsa mapiri pa chigwa ..nzeru zopezela ndalama zatha ku boma Munthu yekha yemwe amaganizila kuphazi osati ubongo ndiye…

Read More
  • Chichewa
  • World

Zisatikhuze MEC ikanila a Police nkhani ya Mithi

admin3 months ago3 months ago03 mins

Bungwe la za chisankho mdziko la Malawi (Malawi Electoral Commission) lawuza bwalo la milandu ku Lilongwe kuti silinakadandaule kuli konse pa zomwe mkulu wodziwika pa masamba a mchezo a Facebook…

Read More
  • Chichewa
  • Politics
  • World

MCP isintha zisankho kuti zikomele nduna- Opikisana

admin3 months ago3 months ago03 mins

Anthu omwe akupikisana mmadela omwe muli zinduna kapena aphungu kale a chipani cholamula cha Malawi Congress (MCP) adandaula kuti masankho osankha oti azayimile pa zisankho za aphungu aku nyumba ya…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

Chakwera adabwitsa anthu pa za katangale

admin4 months ago4 months ago06 mins

President Lazarus Chakwera wadabwitsa a Malawi pomwe anati iye akulimbana ndi katangale zomwe anthu ena sakukondwa nazo. Anthu ambiri pa tsamba la mchezo adabwa naye mtsogoleri wa dziko linoyi ngati…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

 NOCMA, MERA akolezera chipwirikiti cha mafuta: Kampani ya Addax itchulidwa  

admin6 months ago6 months ago018 mins

Zadziwika kuti kampani yoyenga mafuta ya Addax Petroleum ndiyo inatumiza mkulu wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) a Henry Kachaje kupita ku Dubai kuti akachite zokambirana ndi mtsogoleri…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

Ku Balaka njala yavuta

admin2 years ago2 years ago03 mins

..anthu akugona ku Admarc Pamene boma kudzela ku unduna wa za ulimi likuziguguda pa ntima kuti likuthana ndi njala, ku Balaka anthu akugona ku nsika wa Admarc kudikila chimanga chomwe…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

Feteleza kulibe, atelo anthu

admin2 years ago2 years ago08 mins

…feteleza mwalandira- Sam Kawale …Ombudsman akwiya ndi chipwirikiti Pamene nduna ya zaulimi a Sam Kawale amawuza atolankhani ku Lilongwe kuti ntchito yogawa zipangizo za ulimi yayenda bwino, anthu aku Ulongwe…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

MEC iyamba kukonzekera zisankho  za 2025

admin2 years ago2 years ago016 mins

….A Chilima akuzadziwa ngati akudzayima pa 18 Juni, 2025 …Nyumba ya Malamulo ikudzayimitsidwa pa 16 Juni, 2025 …Kalembera wapadera achitika mu Novembala Nthawi yokonzekera chisankho cha mu 2025 yayambika pamene…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

MCP, UTM achotsana ma kholingo ku Blantyre

admin2 years ago2 years ago02 mins

Anyamata otsatila zipani zomwe zili mgwirizano wa Tonse a Malawi Congress ndi UTM lachitatu sabata ino anakokana ma kholingo ndi kuswana ku malo aza malonda ku Chichiri mu mzinda wa…

Read More
  • Chichewa
  • Languages
  • World

Miyala ya Nobium ku Mzimba afuna ayambe kukumba

admin2 years ago2 years ago02 mins

Phindu lake ndi lotani? Kingsley Jassi walemba izi pa tsamba lake la mchezo Patatha zaka 8 boma likukambirana ndi company ya Globe Metals zotsekula mgodi wa Kanyika Niobium ku Mzimba,…

Read More
  • 1
  • 2

Recent Posts

  • Malawi 2025: Women Register to Vote, Men Register Excuses
  • International Conservetionists shocked with Chakweras pardon of criminil gangs
  • UK Sattar’s case set for  Sept 2027
  • Tungwa’s Talking Pen
  • FIRE CHING’OMA, YOLAMU!

Subscribe to our Online Magazine

Recent Posts

  • Malawi 2025: Women Register to Vote, Men Register Excuses
  • International Conservetionists shocked with Chakweras pardon of criminil gangs
  • UK Sattar’s case set for  Sept 2027
  • Tungwa’s Talking Pen
  • FIRE CHING’OMA, YOLAMU!