Apanga phwando ndi infa za Covid

Phase 1 of the Covid-19 vaccination program at Mbagathi Hospital, in Nairobi, Kenya, on April 12, 2021. This first phase is allowed for teachers, health care workers, uniformed forces, administration personnal, religious instructors, clergy, and population with 58 years and above. This phase (and te vaccination program) started in march 9, and the vaccine they are using is the Indian variant of AstraZeneca, called Covishield. (Photo by Robert Bonet/NurPhoto via AP)

Pamene a Malawi anali kulira chifukwa cha imfa za abale awo ku mliri wa Covid, anthu ogwira ntchito za boma anali pa chiphwando kugawana ndalama za Covid. Ombusdman Grace Malera anatulutsa lipoti lomwe likuwonetsa komwe ndalama za Covid zinalowela pomwe ena anali kuthatha ndi moyo.

Welengani nkhaniyi mu Chichewa, mu Chitumbuka ndinso mu chi Yao mmagazine ya The Investigator yomwe yatuluka lero……

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *