Pamene a Malawi anali kulira chifukwa cha imfa za abale awo ku mliri wa Covid, anthu ogwira ntchito za boma anali pa chiphwando kugawana ndalama za Covid. Ombusdman Grace Malera anatulutsa lipoti lomwe likuwonetsa komwe ndalama za Covid zinalowela pomwe ena anali kuthatha ndi moyo.
Welengani nkhaniyi mu Chichewa, mu Chitumbuka ndinso mu chi Yao mmagazine ya The Investigator yomwe yatuluka lero……