Mpingo wa Katolika upeleka za mmbale zonse kwa ovutika ndi Cyclone
Mpingo wa Katoloka wati ndalama ndi zopeleka zonse zilandile la Mulungu sabata ino azipeleka kwa anthu omwe akhuzidwa ndi cyclone Freddy. Mkulu wa bungwe la ma Bishop a Katolika (Episcopal...