MCP, UTM achotsana ma kholingo ku Blantyre
Anyamata otsatila zipani zomwe zili mgwirizano wa Tonse a Malawi Congress ndi UTM lachitatu sabata ino anakokana ma kholingo ndi kuswana ku malo aza malonda ku Chichiri mu mzinda wa…
Anyamata otsatila zipani zomwe zili mgwirizano wa Tonse a Malawi Congress ndi UTM lachitatu sabata ino anakokana ma kholingo ndi kuswana ku malo aza malonda ku Chichiri mu mzinda wa…
Phindu lake ndi lotani? Kingsley Jassi walemba izi pa tsamba lake la mchezo Patatha zaka 8 boma likukambirana ndi company ya Globe Metals zotsekula mgodi wa Kanyika Niobium ku Mzimba,…
Mpingo wa Katoloka wati ndalama ndi zopeleka zonse zilandile la Mulungu sabata ino azipeleka kwa anthu omwe akhuzidwa ndi cyclone Freddy. Mkulu wa bungwe la ma Bishop a Katolika (Episcopal…
Mathews Malata Bungwe la African Parks lonwe likuthandiza boma kusamalira nkhalango za Majete, Liwonde ndi Nkhotakota lati likulingalira zopempha boma kuti liyambe kugwiritsa ntchito ndondomeko “yakulera” pa mikango yomwe ati…
Pamene a Malawi anali kulira chifukwa cha imfa za abale awo ku mliri wa Covid, anthu ogwira ntchito za boma anali pa chiphwando kugawana ndalama za Covid. Ombusdman Grace Malera anatulutsa…