…Chakwera apeza 33.5% The Investigator Magazine itha kulengeza tsopano kuti mtsogoleri wakale wa dziko la Malawi a Peter Mutharika apambana...
Chichewa
Pitani, kaberekani, MCP ilipira. Izi si Malembo Oyera ayi, koma ndilo lonjezo latsopano kwambiri m’ndondomeko ya MCP ya kampeni yakuti a...
..fodya chaka chino wochepa kale ndi 60 million kgs …25% yotenga boma idzutsa mapiri pa chigwa ..nzeru zopezela ndalama zatha...
Bungwe la za chisankho mdziko la Malawi (Malawi Electoral Commission) lawuza bwalo la milandu ku Lilongwe kuti silinakadandaule kuli konse...
Anthu omwe akupikisana mmadela omwe muli zinduna kapena aphungu kale a chipani cholamula cha Malawi Congress (MCP) adandaula kuti masankho...
President Lazarus Chakwera wadabwitsa a Malawi pomwe anati iye akulimbana ndi katangale zomwe anthu ena sakukondwa nazo. Anthu ambiri pa...
Zadziwika kuti kampani yoyenga mafuta ya Addax Petroleum ndiyo inatumiza mkulu wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) a...
..anthu akugona ku Admarc Pamene boma kudzela ku unduna wa za ulimi likuziguguda pa ntima kuti likuthana ndi njala, ku...
...feteleza mwalandira- Sam Kawale ...Ombudsman akwiya ndi chipwirikiti Pamene nduna ya zaulimi a Sam Kawale amawuza atolankhani ku Lilongwe kuti...
….A Chilima akuzadziwa ngati akudzayima pa 18 Juni, 2025 …Nyumba ya Malamulo ikudzayimitsidwa pa 16 Juni, 2025 …Kalembera wapadera achitika...
